Ekisodo 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi ana a Isiraeli anadutsa pakati pa nyanja, panthaka youma,+ madziwo ataima ngati khoma* kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+ Salimo 66:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anasandutsa nyanja kukhala malo ouma,+Anthu anawoloka mtsinje mwa kuyenda ndi mapazi awo.+Pamenepo tinayamba kusangalala mwa iye.+
22 Patapita nthawi ana a Isiraeli anadutsa pakati pa nyanja, panthaka youma,+ madziwo ataima ngati khoma* kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+
6 Anasandutsa nyanja kukhala malo ouma,+Anthu anawoloka mtsinje mwa kuyenda ndi mapazi awo.+Pamenepo tinayamba kusangalala mwa iye.+