Numeri 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+ Numeri 14:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma Mose anati: “N’chifukwa chiyani mukuphwanya lamulo la Yehova?+ Zimenezo sizikuthandizani.
11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+