Yoswa 21:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Choncho Yehova anapatsa Aisiraeli dziko lonse limene analumbira kuti adzapatsa makolo awo,+ ndipo iwo analanda+ dzikolo n’kumakhalamo.
43 Choncho Yehova anapatsa Aisiraeli dziko lonse limene analumbira kuti adzapatsa makolo awo,+ ndipo iwo analanda+ dzikolo n’kumakhalamo.