1 Mafumu 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 inuyo mumve muli kumwamba ndipo mukhululuke tchimo la anthu anu Aisiraeli,+ ndi kuwabwezeretsa+ kudziko limene munapatsa makolo awo.+ 1 Mafumu 8:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 inuyo mumve muli kumwamba,+ malo anu okhala okhazikika+ ndipo mukhululuke+ ndi kuchitapo kanthu.+ Mupatse aliyense malinga ndi njira zake zonse,+ popeza mukudziwa mtima wake+ (popeza inuyo nokha mumadziwa bwino mtima wa ana onse a anthu).+
34 inuyo mumve muli kumwamba ndipo mukhululuke tchimo la anthu anu Aisiraeli,+ ndi kuwabwezeretsa+ kudziko limene munapatsa makolo awo.+
39 inuyo mumve muli kumwamba,+ malo anu okhala okhazikika+ ndipo mukhululuke+ ndi kuchitapo kanthu.+ Mupatse aliyense malinga ndi njira zake zonse,+ popeza mukudziwa mtima wake+ (popeza inuyo nokha mumadziwa bwino mtima wa ana onse a anthu).+