Nehemiya 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’masiku a Eliyasibu,+ Yoyada,+ Yohanani ndi Yaduwa,+ mayina a Alevi komanso ansembe anali kuwalemba m’gulu la atsogoleri a nyumba za makolo mpaka kudzafika m’nthawi ya ufumu wa Dariyo Mperisiya.
22 M’masiku a Eliyasibu,+ Yoyada,+ Yohanani ndi Yaduwa,+ mayina a Alevi komanso ansembe anali kuwalemba m’gulu la atsogoleri a nyumba za makolo mpaka kudzafika m’nthawi ya ufumu wa Dariyo Mperisiya.