Nehemiya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yoyada mwana wamwamuna wa Paseya, komanso Mesulamu mwana wamwamuna wa Besodeya, anakonza Chipata cha Mzinda Wakale.+ Iwo anachipangira felemu lamatabwa ndi kuika zitseko zake, akapichi ake ndi mipiringidzo yake.+
6 Ndiyeno Yoyada mwana wamwamuna wa Paseya, komanso Mesulamu mwana wamwamuna wa Besodeya, anakonza Chipata cha Mzinda Wakale.+ Iwo anachipangira felemu lamatabwa ndi kuika zitseko zake, akapichi ake ndi mipiringidzo yake.+