Ezara 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero anthu sanathe kusiyanitsa phokoso lawo losonyeza kusangalala+ ndi losonyeza kulira, chifukwa anthuwo anali kufuula kwambiri, ndipo phokoso lawo linali kumveka kutali kwambiri.
13 Chotero anthu sanathe kusiyanitsa phokoso lawo losonyeza kusangalala+ ndi losonyeza kulira, chifukwa anthuwo anali kufuula kwambiri, ndipo phokoso lawo linali kumveka kutali kwambiri.