3 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando+ akalonga ndi atumiki ake onse, akuluakulu a asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka+ ndi akalonga a m’zigawo za ufumu wake.+
16 Pamenepo anatenga Esitere kupita naye kwa Mfumu Ahasiwero, kunyumba yake yachifumu, m’mwezi wa 10 umene ndi mwezi wa Tebeti,* m’chaka cha 7+ cha ulamuliro wa Mfumu Ahasiwero.