Esitere 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akalonga onse+ a m’zigawozo, masatarapi,*+ abwanamkubwa ndi onse ogwira ntchito+ za mfumu anali kuthandiza Ayudawo chifukwa anali kuopa+ Moredekai.
3 Akalonga onse+ a m’zigawozo, masatarapi,*+ abwanamkubwa ndi onse ogwira ntchito+ za mfumu anali kuthandiza Ayudawo chifukwa anali kuopa+ Moredekai.