Esitere 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi yomweyo mfumu inauza Hamani kuti: “Fulumira, tenga chovala ndi hatchi monga mmene wanenera, ndipo ukachitire zimenezi Moredekai, Myuda, amene ali kuchipata. Uonetsetse kuti zonse zimene wanenazi zakwaniritsidwa.”+
10 Nthawi yomweyo mfumu inauza Hamani kuti: “Fulumira, tenga chovala ndi hatchi monga mmene wanenera, ndipo ukachitire zimenezi Moredekai, Myuda, amene ali kuchipata. Uonetsetse kuti zonse zimene wanenazi zakwaniritsidwa.”+