Esitere 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako mfumu inamufunsa kuti: “Chavuta n’chiyani Mfumukazi Esitere, ndipo ukufuna kupempha chiyani?+ Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.”
3 Kenako mfumu inamufunsa kuti: “Chavuta n’chiyani Mfumukazi Esitere, ndipo ukufuna kupempha chiyani?+ Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.”