Esitere 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ayuda anasonkhana pamodzi+ m’mizinda yawo m’zigawo zonse za Mfumu Ahasiwero+ kuti agwire anthu amene anali kufuna kuwachitira zinthu zoipa.+ Ndipo palibe munthu amene analimba mtima pamaso pawo chifukwa anthu a mitundu yonse anali kuopa+ Ayudawo.
2 Ayuda anasonkhana pamodzi+ m’mizinda yawo m’zigawo zonse za Mfumu Ahasiwero+ kuti agwire anthu amene anali kufuna kuwachitira zinthu zoipa.+ Ndipo palibe munthu amene analimba mtima pamaso pawo chifukwa anthu a mitundu yonse anali kuopa+ Ayudawo.