Esitere 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 pa tsiku la 13 la mwezi wa Adara. Ndiyeno pa tsiku la 14 la mweziwo anapuma ndi kulisandutsa tsiku laphwando+ ndi lachikondwerero.+ Esitere 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’makalatawo anawalamula kuti pa tsiku la 14 ndi la 15 la mwezi wa Adara azichita+ chikondwerero chimenechi nthawi zonse chaka ndi chaka.
17 pa tsiku la 13 la mwezi wa Adara. Ndiyeno pa tsiku la 14 la mweziwo anapuma ndi kulisandutsa tsiku laphwando+ ndi lachikondwerero.+
21 M’makalatawo anawalamula kuti pa tsiku la 14 ndi la 15 la mwezi wa Adara azichita+ chikondwerero chimenechi nthawi zonse chaka ndi chaka.