Esitere 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ayuda ena onse amene anali m’zigawo+ za mfumu anasonkhana pamodzi kuti ateteze miyoyo yawo.+ Ndipo anabwezera+ adani awo ndi kupha anthu 75,000 amene anali kudana nawo, koma sanafunkhe zinthu zawo
16 Ayuda ena onse amene anali m’zigawo+ za mfumu anasonkhana pamodzi kuti ateteze miyoyo yawo.+ Ndipo anabwezera+ adani awo ndi kupha anthu 75,000 amene anali kudana nawo, koma sanafunkhe zinthu zawo