Deuteronomo 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo amuna onse a mumzinda wawo azim’ponya miyala ndi kumupha. Muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha kwambiri.+ Esitere 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Esitere anati: “Ngati zingakukomereni mfumu,+ lolani kuti mawa Ayuda amene ali mu Susani achite mogwirizana ndi zimene lamulo laleroli likunena.+ Lolani kuti ana aamuna 10 a Hamani apachikidwe pamtengo.”+
21 Pamenepo amuna onse a mumzinda wawo azim’ponya miyala ndi kumupha. Muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha kwambiri.+
13 Pamenepo Esitere anati: “Ngati zingakukomereni mfumu,+ lolani kuti mawa Ayuda amene ali mu Susani achite mogwirizana ndi zimene lamulo laleroli likunena.+ Lolani kuti ana aamuna 10 a Hamani apachikidwe pamtengo.”+