Ekisodo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+ 1 Samueli 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anayankha kuti: “Inde, n’kwabwino. Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova. Dziyeretseni,+ ndipo mupite nane kopereka nsembe.” Chotero iye anayeretsa Jese ndi ana ake, kenako anawaitanira kopereka nsembe.
10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+
5 Iye anayankha kuti: “Inde, n’kwabwino. Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova. Dziyeretseni,+ ndipo mupite nane kopereka nsembe.” Chotero iye anayeretsa Jese ndi ana ake, kenako anawaitanira kopereka nsembe.