Miyambo 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mphepo yochokera kumpoto imabweretsa mvula yambiri. Imakhala ngati kuti yabereka mvulayo ndi ululu wa pobereka.+ Chotero munthu wa lilime loulula chinsinsi amakhala ndi nkhope yonyozedwa.+
23 Mphepo yochokera kumpoto imabweretsa mvula yambiri. Imakhala ngati kuti yabereka mvulayo ndi ululu wa pobereka.+ Chotero munthu wa lilime loulula chinsinsi amakhala ndi nkhope yonyozedwa.+