Yobu 42:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu munati, ‘Tamvera, ndikufuna ndikulankhule.Ndikufunsa mafunso ndipo iweyo undiyankhe.’+