Yakobo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Paja tonsefe timapunthwa nthawi zambiri.+ Ngati wina sapunthwa pa mawu,+ ameneyo ndi munthu wangwiro,+ ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.
2 Paja tonsefe timapunthwa nthawi zambiri.+ Ngati wina sapunthwa pa mawu,+ ameneyo ndi munthu wangwiro,+ ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.