Salimo 88:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mafunde a mkwiyo wanu woyaka moto andimiza.+Zinthu zochititsa mantha zochokera kwa inu zandisowetsa chonena.+
16 Mafunde a mkwiyo wanu woyaka moto andimiza.+Zinthu zochititsa mantha zochokera kwa inu zandisowetsa chonena.+