Yobu 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amuna onse amene anali anzanga apamtima akudana nane,+Ndipo amene ndinali kuwakonda anditembenukira.+ Salimo 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+
19 Amuna onse amene anali anzanga apamtima akudana nane,+Ndipo amene ndinali kuwakonda anditembenukira.+
11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+