Genesis 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero anapulumutsa katundu wawo yense.+ Anapulumutsanso Loti m’bale wake, katundu wake, akazi, ndi anthu ena.+
16 Atatero anapulumutsa katundu wawo yense.+ Anapulumutsanso Loti m’bale wake, katundu wake, akazi, ndi anthu ena.+