Yobu 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho, sindingamuyankhe ngakhale nditakhala kuti ndikunena zoona.+Ndingachonderere amene akutsutsana nane pa mlandu.+ Luka 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chimodzimodzi inunso, mukachita zonse zimene munapatsidwa ngati ntchito yanu, muzinena kuti, ‘Ife ndife akapolo opanda pake.+ Tangochita zimene tinayenera kuchita.’”
15 Choncho, sindingamuyankhe ngakhale nditakhala kuti ndikunena zoona.+Ndingachonderere amene akutsutsana nane pa mlandu.+
10 Chimodzimodzi inunso, mukachita zonse zimene munapatsidwa ngati ntchito yanu, muzinena kuti, ‘Ife ndife akapolo opanda pake.+ Tangochita zimene tinayenera kuchita.’”