Salimo 39:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Inu Yehova, ndidziwitseni za kufulumira kwa chimaliziro changa,+Ndiponso kuti masiku anga ndi ochepa motani,+Kuti ndidziwe kufupika kwa moyo wanga.+ Luka 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako adzaufuna.+ Nanga chuma chimene waunjikachi chidzakhala cha ndani?’+
4 “Inu Yehova, ndidziwitseni za kufulumira kwa chimaliziro changa,+Ndiponso kuti masiku anga ndi ochepa motani,+Kuti ndidziwe kufupika kwa moyo wanga.+
20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako adzaufuna.+ Nanga chuma chimene waunjikachi chidzakhala cha ndani?’+