Yobu 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndamva zinthu zambiri ngati zimenezi.Nonsenu ndinu otonthoza onditopetsa!+ Yobu 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova atanena mawu amenewa kwa Yobu, Yehovayo anauza Elifazi wa ku Temani kuti:“Mkwiyo wanga wayakira iweyo ndi anzako awiriwo+ chifukwa inu simunanene zoona za ine,+ monga wachitira Yobu mtumiki wanga.
7 Yehova atanena mawu amenewa kwa Yobu, Yehovayo anauza Elifazi wa ku Temani kuti:“Mkwiyo wanga wayakira iweyo ndi anzako awiriwo+ chifukwa inu simunanene zoona za ine,+ monga wachitira Yobu mtumiki wanga.