1 Atesalonika 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pewani zoipa zamtundu uliwonse.+ 1 Petulo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 koma aleke zoipa+ ndipo achite zabwino. Ayesetse kupeza mtendere ndi kuusunga.+