-
Yobu 42:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Chotero Elifazi wa ku Temani, Bilidadi wa ku Shuwa ndi Zofari wa ku Naama anapita n’kukachita monga mmene Yehova anawauzira. Choncho Yehova anamva pemphero la Yobu.
-