Yobu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye waika abale anga enieni kutali ndi ine,+Ndipo ngakhale anthu ondidziwa andisiya.