Genesis 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako, Yakobo ananyamuka n’kupitiriza ulendo wake wopita Kum’mawa.+ 1 Mafumu 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Nzeru za Solomo zinaposa+ nzeru za anthu onse a Kum’mawa+ ndi nzeru zonse za ku Iguputo.+