Yobu 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti ndikudziwa bwino kuti mudzandibwezera ku imfa,+Kunyumba yosonkhanako aliyense wamoyo. Yohane 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atanena zimenezi, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Bwenzi lathu Lazaro ali m’tulo akupumula, koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa ku tulo take.”+
11 Atanena zimenezi, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Bwenzi lathu Lazaro ali m’tulo akupumula, koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa ku tulo take.”+