Yobu 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nanga kuli bwanji munthu wonyansa ndi woipa,+Munthu yemwe amamwa zosalungama ngati madzi? Mateyu 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Usalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenya mbama patsaya lakumanja,+ umutembenuzirenso linalo.
39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Usalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenya mbama patsaya lakumanja,+ umutembenuzirenso linalo.