Salimo 147:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova amasangalala ndi anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha.+