Machitidwe 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma chapakati pa usiku,+ Paulo ndi Sila anali kupemphera ndi kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ ndipo akaidi ena anali kuwamva. Aefeso 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu. Nthawi zonse muziyamika+ Mulungu, Atate wathu, pa zinthu zonse.
25 Koma chapakati pa usiku,+ Paulo ndi Sila anali kupemphera ndi kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ ndipo akaidi ena anali kuwamva.
20 m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu. Nthawi zonse muziyamika+ Mulungu, Atate wathu, pa zinthu zonse.