Yeremiya 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ansembe ndidzawatsitsimutsa ndi chakudya chochuluka,+ ndipo anthu anga ndidzawakhutiritsa ndi ubwino wanga,”+ watero Yehova. 1 Petulo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 pakuti mwalawa n’kuona kuti Ambuye ndi wokoma mtima.+
14 Ansembe ndidzawatsitsimutsa ndi chakudya chochuluka,+ ndipo anthu anga ndidzawakhutiritsa ndi ubwino wanga,”+ watero Yehova.