Salimo 115:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzadalitsa anthu omuopa,+Adzadalitsa onsewo osasiyapo aliyense.+ Miyambo 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Madalitso amapita pamutu pa wolungama,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamabisa zachiwawa.+