Salimo 89:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndinaphwanya adani ake zidutswazidutswa ndi kuwachotsa pamaso pake,+Ndipo odana naye kwambiri ndinapitirizabe kuwamenya.+ Yohane 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lilibe chifukwa chodana ndi inu, koma limadana ndi ine, chifukwa ndimachitira umboni kuti dzikoli ntchito zake ndi zoipa.+
23 Ndinaphwanya adani ake zidutswazidutswa ndi kuwachotsa pamaso pake,+Ndipo odana naye kwambiri ndinapitirizabe kuwamenya.+
7 Dziko lilibe chifukwa chodana ndi inu, koma limadana ndi ine, chifukwa ndimachitira umboni kuti dzikoli ntchito zake ndi zoipa.+