Salimo 71:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti adani anga anena za ine,+Ndipo anthu olondalonda moyo wanga, onse pamodzi achita upo,+