Salimo 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+ Miyambo 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usamapse mtima chifukwa cha anthu ochita zoipa. Usamasirire anthu oipa,+
7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+