Yesaya 58:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 pamenepo mudzasangalala kwambiri mwa Yehova.+ Ine ndidzakuchititsani kuti mukwere m’malo okwezeka a dziko lapansi,+ ndipo ndidzakuchititsani kuti mudye zochokera m’cholowa cha Yakobo kholo lanu,+ pakuti pakamwa pa Yehova panena zimenezi.”+
14 pamenepo mudzasangalala kwambiri mwa Yehova.+ Ine ndidzakuchititsani kuti mukwere m’malo okwezeka a dziko lapansi,+ ndipo ndidzakuchititsani kuti mudye zochokera m’cholowa cha Yakobo kholo lanu,+ pakuti pakamwa pa Yehova panena zimenezi.”+