Yobu 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Oipawo amakhala okwezeka kwa kanthawi, kenako n’kutha.+Iwo amatsitsidwa,+ ndipo mofanana ndi wina aliyense amathotholedwa.Amadulidwa mofanana ndi nsonga ya ngala za tirigu. Aheberi 10:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pakuti “kwatsala kanthawi kochepa kwambiri,”+ ndipo “amene akubwerayo afika ndithu, sachedwa ayi.”+ 1 Petulo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira.+ Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+
24 Oipawo amakhala okwezeka kwa kanthawi, kenako n’kutha.+Iwo amatsitsidwa,+ ndipo mofanana ndi wina aliyense amathotholedwa.Amadulidwa mofanana ndi nsonga ya ngala za tirigu.
37 Pakuti “kwatsala kanthawi kochepa kwambiri,”+ ndipo “amene akubwerayo afika ndithu, sachedwa ayi.”+
7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira.+ Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+