Salimo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Yehova, musandidzudzule mutakwiya.+Musandiwongolere mutapsa mtima.+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+
6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+