Mateyu 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Bwerani kwa ine nonsenu ogwira ntchito yolemetsa ndi olemedwa,+ ndipo ndidzakutsitsimutsani.