2 Samueli 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Davide anapitiriza kuuza Abisai ndi atumiki ake onse kuti: “Ngati mwana wanga weniweni, wotuluka m’chiuno mwanga akufunafuna moyo wanga,+ kuli bwanji M’benjamini uyu!+ Musiyeni anyoze, pakuti Yehova wamuuza kuti atero!
11 Ndiyeno Davide anapitiriza kuuza Abisai ndi atumiki ake onse kuti: “Ngati mwana wanga weniweni, wotuluka m’chiuno mwanga akufunafuna moyo wanga,+ kuli bwanji M’benjamini uyu!+ Musiyeni anyoze, pakuti Yehova wamuuza kuti atero!