Salimo 37:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+
39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+