Salimo 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+ Salimo 71:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ine ndidzayembekezera inu nthawi zonse,+Ndipo ndidzakutamandani mowirikiza kuposa kale.
7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+