Yobu 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mapazi anga amatsata mayendedwe ake.Ndasunga njira yake, ndipo sindipatukapo.+ Salimo 119:157 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 157 Anthu ondizunza komanso adani anga ndi ambiri.+Koma ine sindinapatuke pa zikumbutso zanu.+