Salimo 79:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Apereka mitembo ya atumiki anu kwa mbalame kuti chikhale chakudya chawo.+Matupi a okhulupirika anu awapereka kwa zilombo zakutchire.+ Aroma 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+
2 Apereka mitembo ya atumiki anu kwa mbalame kuti chikhale chakudya chawo.+Matupi a okhulupirika anu awapereka kwa zilombo zakutchire.+
36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+