2 Samueli 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzimu wa Yehova unandilankhulitsa,+Ndipo mawu ake anali palilime langa.+ Yesaya 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova anandiuza kuti: “Tenga cholembapo chachikulu+ ndipo ulembepo ndi cholembera wamba, kuti: ‘Maheri-salala-hasi-bazi.’* Yeremiya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Anthu inu munganene bwanji kuti: “Ndife anzeru, ndipo tili ndi chilamulo cha Yehova”?+ Ndithudi, zolembera zachinyengo+ za alembi zagwiritsidwa ntchito mwachinyengo.
8 Yehova anandiuza kuti: “Tenga cholembapo chachikulu+ ndipo ulembepo ndi cholembera wamba, kuti: ‘Maheri-salala-hasi-bazi.’*
8 “‘Anthu inu munganene bwanji kuti: “Ndife anzeru, ndipo tili ndi chilamulo cha Yehova”?+ Ndithudi, zolembera zachinyengo+ za alembi zagwiritsidwa ntchito mwachinyengo.