Nyimbo ya Solomo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ngati iweyo sukudziwa, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse,+ tsatira mapazi a ziweto ndipo ukadyetse ana ako a mbuzi pafupi ndi mahema a abusa.” Nyimbo ya Solomo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Monga duwa pakati pa zitsamba zaminga, ndi mmene alili wokondedwa wanga pakati pa ana aakazi.”+
8 “Ngati iweyo sukudziwa, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse,+ tsatira mapazi a ziweto ndipo ukadyetse ana ako a mbuzi pafupi ndi mahema a abusa.”