Chivumbulutso 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+ Chivumbulutso 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+
8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+
2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+